Mawu a M'munsi
c N’kutheka kuti timeneti tinali tinsalu timene Paulo ankamanga pachipumi kuti thukuta lisamayenderere n’kulowa m’maso. Komanso mfundo yakuti Paulo ankavala maepuloni ikusonyeza kuti iye ankagwira ntchito yake yokonza matenti pa nthawi yake yopuma, mwina m’mawa kwambiri.—Mac. 20:34, 35.