Mawu a M'munsi b Zikuoneka kuti Paulo analemba kalata yopita kwa Aroma pa nthawi imeneyi pamene anali ku Korinto.