Mawu a M'munsi
d Pa Machitidwe 20:5, 6 Luka anagwiritsa ntchito mawu akuti “ankatiyembekezera” komanso akuti “tinawapeza,” omwe akusonyeza kuti anali limodzi ndi Paulo. N’kutheka kuti anakumananso ndi Paulo ku Filipi, chifukwa Paulo anamusiya mumzinda umenewu m’mbuyomu.—Mac. 16:10-17, 40.