Mawu a M'munsi
e Abalewo anayenda ulendo wapanyanja kwa masiku 5 kuchoka ku Filipi kupita ku Torowa. Zimenezi zikusonyeza kuti mwina panyanjapo panali mphepo yamkuntho chifukwa m’mbuyomu, iwo anayenda ulendo womwewu kwa masiku awiri okha.—Mac. 16:11.