Mawu a M'munsi
a Anaziri anali anthu amene ankalonjeza kuti pa moyo wawo sazichita zinthu zina. Zimenezi zinkaphatikizapo kuti sadzamwa chakumwa chilichonse choledzeretsa ndiponso sadzameta tsitsi lawo. Anthu ambiri ankalonjeza kuti akhala Anaziri kwa kanthawi ndipo ndi anthu ochepa okha monga Samisoni, Samueli ndi Yohane M’batizi amene anakhala Anaziri kwa moyo wawo wonse.