Mawu a M'munsi a Karimeli ameneyu si phiri lotchuka lomwe linali kumpoto kwambiri kwa Maoni komwe pambuyo pake mneneri Eliya anakumana ndi aneneri a Baala. (Onani Mutu 10.) Koma unali mudzi womwe unali kufupi ndi chipululu cha Parana.