Mawu a M'munsi
a Zimenezi zitangochitika, Yehova anauza Eliya kuti aphunzitse ntchito Elisa, yemwe anadzakhala ‘wothirira Eliya madzi osamba m’manja.’ (2 Maf. 3:11) Elisa anakhala mtumiki wa Eliya ndipo ayenera kuti ankamuthandiza pa zinthu zina ndi zina popeza anali wachikulire.