Mawu a M'munsi
a Kuchokera mu 455 B.C.E. kufika mu 1 B.C.E. ndi zaka 454. Kuchokera mu 1 B.C.E. kufika mu 1 C.E. ndi chaka chimodzi. Ndipo kuchokera mu 1 C.E. kufika mu 29 C.E. ndi zaka 28. Choncho tikaphatikiza zakazi (454 + 1 + 28) tikupeza zaka 483.