Mawu a M'munsi
a M’zipembedzo zina amanena kuti kutchula dzina la Mulungu, ngakhale popemphera, n’kulakwa. Koma dzina limenelo limapezeka maulendo pafupifupi 7,000 m’zinenero zoyambirira za Baibulo. Kawirikawiri dzinali limapezeka m’mapemphero ndi mu nyimbo zotamanda Mulungu za atumiki okhulupirika a Yehova.