Mawu a M'munsi
a Zikuoneka kuti Yehova ankafuna kuti atumwiwo adzakhale ‘miyala yokwana 12 yomangira maziko’ a Yerusalemu Watsopano. (Chiv. 21:14) Choncho kuchokera nthawi imeneyi panalibe chifukwa choti mtumwi wokhulupirika aliyense akamwalira, azilowedwa m’malo.