Mawu a M'munsi
a Munkhaniyi, mawu oti “anthu othawa kwawo” akunena za anthu amene athawa m’dziko lawo kapena m’dera lawo chifukwa cha nkhondo, kuzunzidwa kapena ngozi inayake. Nthambi ya bungwe la United Nations yoona za anthu othawa kwawo (UNHCR) inanena kuti masiku ano “munthu mmodzi pa anthu 113 alionse amathawa kwawo.”