Mawu a M'munsi
b Pofuna kutithandiza kukhala ndi mtima wofuna kuimba, msonkhano wadera kapena wachigawo umayamba ndi kumvetsera nyimbo kwa 10 minitsi. Nyimbozi zimakonzedwa m’njira yoti zitithandize kukonzekeretsa mitima yathu kuti tipindule ndi nkhani zomwe zikambidwe. Choncho nyimbozi zikangoyamba, tingachite bwino kukhala m’mipando yathu n’kumamvetsera.