Mawu a M'munsi
a Baibulo limasonyeza kuti angelo ena ali ndi mayina awo enieni. (Ower. 13:18; Dan. 8:16; Luka 1:19; Chiv. 12:7) Koma popeza Yehova amatchula dzina nyenyezi iliyonse, (Sal. 147:4) n’zomveka kunena kuti angelo onse, kuphatikizapo amene anadzakhala Satana, ali ndi mayina.