Mawu a M'munsi a Katswiri wa mbiri ya Ayuda dzina lake Josephus ananena kuti pa nthawiyi Samueli anali ndi zaka 12.