Mawu a M'munsi
b N’zodziwikiratu kuti anthu ena amene adzapulumuke nkhondo ya Aramagedo adzakhala olumala. Yesu ali padzikoli, anachiritsa anthu okhala ndi “zofooka zilizonse” ndipo zimenezi zikusonyeza zimene iye adzachitire anthu opulumuka pa Aramagedo, osati oukitsidwa. (Mat. 9:35) N’zosakayikitsa kuti anthu amene anamwalira adzaukitsidwa ndi matupi abwinobwino.