Mawu a M'munsi
a Posachedwapa tichita mwambo wa Chikumbutso pokumbukira imfa ya Yesu Khristu. Mwambo wosavutawu umasonyeza kuti Yesu ndi wodzichepetsa, wolimba mtima komanso wachikondi. Munkhaniyi tikambirana zimene tingachite kuti tizitsanzira makhalidwe a Yesuwa.