Mawu a M'munsi
a Mwambo wa Chikumbutso udzachitika Lachisanu pa 19 April 2019, ndipo udzakhala msonkhano wapadera kwambiri pamisonkhano yonse ya chaka chimenechi. Kodi n’chiyani chimatichititsa kupezeka pamsonkhanowu? N’chifukwa chakuti timafuna kusangalatsa Yehova. Munkhaniyi, tikambirana makhalidwe amene amatichititsa kuti tizipezeka pamwambo wa Chikumbutso komanso pamisonkhano ya mlungu uliwonse.