Mawu a M'munsi
c MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI Tsamba 28-29: M’bale ali kundende ndipo walimbikitsidwa kwambiri ndi kalata imene walemberedwa. Iye akuona kuti sanaiwalidwe ndipo akusangalala kumva kuti banja lake lonse ndi lokhulupirikabe ngakhale kuti zinthu sizili bwino m’dera lawo.