Mawu a M'munsi
a Kodi tingaphunzire chiyani kwa Yehova, Yesu komanso wakhate wina wa ku Samariya pa nkhani yoyamikira? Munkhaniyi tikambirana zitsanzo zimenezi komanso zina. Tikambirananso chifukwa chake tiyenera kusonyeza kuyamikira komanso mmene tingachitire zimenezi.