Mawu a M'munsi
a Yehova ndi Yesu amachita zinthu moganizira mmene anthu ena akumvera mumtima mwawo. Munkhaniyi tikambirana zimene tingachite powatsanzira. Tikambirananso chifukwa chake tiyenera kuchita zinthu moganizira ena komanso mmene tingachitire zimenezo.