Mawu a M'munsi
c Yehova anathandizanso mokoma mtima anthu amene ankapwetekedwa kwambiri mtima kapena kuchita mantha. Mwachitsanzo, anathandiza Hana (1 Sam. 1:10-20), Eliya (1 Maf. 19:1-18) komanso Ebedi-meleki (Yer. 38:7-13; 39:15-18).