Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Tikapita kumisonkhano timakhala ndi mwayi wocheza ndi anthu. Pachithunzipa pali (1) mkulu akulankhula ndi kamnyamata komanso mayi ake, (2) bambo ndi mwana wawo akuthandiza mlongo wachikulire kuti akakwere galimoto, (3) akulu awiri akumvetsera bwino pamene mlongo akupempha malangizo pa vuto lake.