Mawu a M'munsi
a Yesu ali padzikoli, Yehova analankhula katatu kuchokera kumwamba. Pa ulendo wina Yehova anauza ophunzira a Khristu kuti azimvera Mwana wake. Masiku ano, Yehova amatilankhula kudzera m’Mawu ake, omwe amaphatikizapo zimene Yesu anaphunzitsa, komanso kudzera m’gulu lake. Munkhaniyi tikambirana ubwino womvera Yehova ndi Yesu.