Mawu a M'munsi
a Tonsefe maganizo athu amakhala ogwirizana ndi kumene tinakulira, chikhalidwe chathu komanso maphunziro athu. Ndipo tikhoza kuzindikira kuti maganizo ena olakwika anatilowerera kwambiri. Munkhaniyi tikambirana zimene tingachite kuti tichotse maganizo olakwika alionse amene tili nawo.