Mawu a M'munsi
b MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Zithunzi zonse zikusonyeza zimene a Mboni akuchita m’dziko limene boma laletsa ntchito yathu. Pachithunzichi anthu ochepa akuchita misonkhano m’chipinda chosungira katundu cha m’bale wina.