Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano

Mawu a M'munsi

b MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Abale akuyeretsa Nyumba ya Ufumu ndipo m’bale wina dzina lake Joe wasiya kaye kuti alankhule ndi m’bale wina ndi mwana wake. Zimene wachitazi zakwiyitsa Mike yemwe akuyeretsanso nawo. Iye akuganiza kuti, ‘Koma zoona Joe akucheza m’malo mogwira ntchito?’ Koma pa nthawi ina, Mike akuona Joe akuthandiza mokoma mtima mlongo wina wachikulire. Zimenezi zakumbutsa Mike kuti ayenera kuyesetsa kuganizira makhalidwe abwino a Joe.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani