Mawu a M'munsi
a Posachedwapa maboma adzalengeza kuti akwanitsa kubweretsa “bata ndi mtendere.” Zimenezi zidzasonyeza kuti chisautso chachikulu chatsala pang’ono kwambiri kuyamba. Koma kodi Yehova amafuna kuti tizichita chiyani panopa? Nkhaniyi iyankha funso limeneli.