Mawu a M'munsi
b MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Sitingakonde kudya chakudya choipitsidwa chomwe chaphikidwa m’khitchini yauve. Ndiye palibe chifukwa choonera zosangalatsa zomwe zaipitsidwa ndi zinthu zachiwawa, kukhulupirira mizimu kapena chiwerewere