Mawu a M'munsi
a Pamene mapeto akuyandikira, tikufunika kumagwirizana kwambiri ndi Akhristu anzathu. Munkhaniyi, tikambirana zimene tingaphunzire pa nkhani ya Yeremiya. Tikambirananso mmene kupeza anzathu apamtima panopa kungatithandizire pa nthawi yamavuto.