Mawu a M'munsi
a Asilikali akale ankadalira chishango kuti atetezeke. Chikhulupiriro chathu chimakhalanso ngati chishango. Ndipo mofanana ndi chishango, chikhulupiriro chathu chimafunika kuchisamalira. Munkhaniyi tiona zimene tingachite kuti tizisamalira ‘chishango chathu chachikulu chachikhulupiriro.’