Mawu a M'munsi
a Malemba amatithandiza kukhala ndi maganizo oyenera pa nkhani ya ntchito komanso kupuma. Nkhaniyi itithandiza kudzifufuza kuti tidziwe mmene timaonera zinthu zimenezi. Ndipo tikambirana pogwiritsa ntchito zimene Aisiraeli ankachita pa Sabata.