Mawu a M'munsi
b Ophunzira a Yesu ankalemekeza kwambiri lamulo la Sabata moti anasiya kupanga zonunkhiritsa zoti akonzere thupi la Yesu mpaka tsiku la Sabata litadutsa.—Luka 23:55, 56.