Mawu a M'munsi
a Kodi anthu a pa banja ayenera kubereka ana? Ngati angasankhe kubereka, kodi ayenera kukhala ndi ana angati? Nanga kodi angaphunzitse bwanji anawo kuti azikonda komanso kutumikira Yehova? Munkhaniyi tikambirana zitsanzo za masiku ano komanso mfundo za m’Baibulo zimene zingatithandize kuyankha mafunso amenewa.