Mawu a M'munsi
c TANTHAUZO LA MAWU ENA: Chidindo. Munthu sadindidwa chidindo chomaliza mpaka atatsala pang’ono kufa adakali wokhulupirika kapena chisautso chachikulu chitatsala pang’ono kuyamba.—Aef. 4:30; Chiv. 7:2-4; onani “Mafunso Ochokera kwa Owerenga” mu Nsanja ya Olonda ya April 2016.