Mawu a M'munsi
a Nthawi zina, tonsefe timakhala ndi nkhawa chifukwa cha mavuto amene timakumana nawo. Munkhaniyi tikambirana za atumiki atatu a Yehova otchulidwa m’Baibulo amene anavutikapo ndi nkhawa. Tikambirananso mmene Yehova anawatonthozera n’kuwathandiza kuti apeze mtendere.