Mawu a M'munsi
b TANTHAUZO LA MAWU ENA: Kuda nkhawa kumatanthauza kuchita mantha kapena kudandaula za zinthu zinazake. Tikhoza kuda nkhawa chifukwa cha mavuto azachuma, matenda, mavuto a m’banja kapena mavuto ena. Tingamadenso nkhawa chifukwa cha zolakwa zimene tinachita m’mbuyo kapena mavuto amene tikuganiza kuti tingadzakumane nawo m’tsogolo.