Mawu a M'munsi
a M’Mawu a Mulungu muli mfundo zotithandiza kudziwa nthawi yoyenera kulankhula ndi yoyenera kukhala chete. Tikadziwa zimene Baibulo limanena pa nkhaniyi n’kumazitsatira, zolankhula zathu zidzakhala zosangalatsa Yehova.