Mawu a M'munsi
b Munkhani za mutu wakuti “Baibulo Limasintha Anthu” muli zitsanzo zambiri za anthu amene anasintha. Nkhani zimenezi zinkapezeka mu Nsanja ya Olonda mpaka mu 2017. Koma panopa zimapezeka pa jw.org®. Pitani pamene alemba kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA.