Mawu a M'munsi
c Kuti mudziwe zinthu zimene zingathandize anthu amene amavutika ndi nkhawa komanso nkhani za anthu amene anakumana ndi vutoli, onerani pulogalamu ya JW Broadcasting® ya May 2019. Pitani pa jw.org®. Pitani pamene alemba kuti LAIBULALE > JW BROADCASTING®.