Mawu a M'munsi
a Yehova akufuna kuti anthu amene anasiya kusonkhana komanso kulalikira abwererenso kwa iye. Yehova akuwauza kuti: “Bwererani kwa ine.” Pali zambiri zomwe tingachite kuti tiwathandize. Munkhaniyi tikambirana zimene tingachite powathandiza kuti abwerere.