Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Abale atatu akuthandiza m’bale amene akufuna kubwerera kwa Yehova. M’bale wina akuchita zimenezi poimbira foni wofookayo, wina akuchita zinthu zosonyeza kuti amamukonda ndipo wina akuyesetsa kumumvetsera ndi kusonyeza kuti akumumvetsa.