Mawu a M'munsi
a Munthu wodzichepetsa amakhala wachifundo komanso wokoma mtima. Choncho n’zomveka kunena kuti Yehova ndi wodzichepetsa. Monga tionere munkhaniyi, tikhoza kuphunzira kudzichepetsa kuchokera kwa Yehova. Tiphunziranso zambiri pankhaniyi kuchokera m’chitsanzo cha Mfumu Sauli, mneneri Danieli komanso Yesu.