Mawu a M'munsi
c MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Mlongo yemwe ndi mpainiya waonera mavidiyo amene akusonyeza anthu ena omwe akutumikira kudera limene kukufunika ofalitsa ambiri. Zimenezi zamulimbikitsa kuti atengere chitsanzo chawo. Kenako nayenso wakwanitsa cholinga chake chomwe ndikukatumikira kudera limene kukufunika ofalitsa ambiri.