Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano

Mawu a M'munsi

a Sikulakwa kuganizira zinthu zimene zinachitika pa moyo wathu m’mbuyomu. Koma tikamaganizira kwambiri zinthu zimenezi, zingatilepheretse kuti tizichita zambiri potumikira Yehova panopa komanso tingaiwale malonjezo abwino amene Yehova watilonjeza. Munkhaniyi tikambirana zinthu zitatu zimene tiyenera kupewa zomwe zingatichititse kuti tiziganizira zinthu zimene zinachitika m’mbuyo. Tikambirananso mmene mfundo za m’Baibulo komanso zitsanzo za abale ndi alongo athu zingatithandizire kupewa zinthu zitatu zimenezi.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani