Mawu a M'munsi
a Muchaputala 15 cha buku la 1 Akorinto, Paulo anafotokoza za kuuka kwa akufa. Kodi nkhani ya kuuka kwa akufa ndi yofunika bwanji kwa ife, nanga n’chifukwa chiyani timakhulupirira kuti Yesu anauka? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa ndi enanso ofunika okhudza kuuka kwa akufa.