Mawu a M'munsi
a Buku la Yakobo lili ndi malangizo ofunika omwe angatithandize tikakumana ndi mayesero. Munkhaniyi tikambirana ena mwa malangizo amene Yakobo anapereka. Malangizo amenewa angatithandize kuti tizipirira tikakumana ndi mavuto n’kumakhalabe osangalala pamene tikutumikira Yehova.