Mawu a M'munsi
a Nkhani zambiri za m’Baibulo zimasonyeza kuti Yehova amakonda atumiki ake ndipo adzapitiriza kuwathandiza akamakumana ndi mayesero. Nkhaniyi itithandiza kuona zimene tingachite kuti tikamaphunzira nkhani za m’Baibulo patokha tizipindula kwambiri.