Mawu a M'munsi
b Imene tafotokozayi ndi imodzi mwa njira zimene mungagwiritse ntchito pophunzira. Njira zina zophunzirira Baibulo mungazipeze mu Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani, pa mutu wakuti “Baibulo” pansi pa kamutu kakuti “Kuwerenga ndi Kumvetsa Bwino Baibulo.”