Mawu a M'munsi
a M’Baibulo, Yehova amatilonjeza kuti adzatipatsa mphamvu komanso kutiteteza ku zinthu zimene zingawononge ubwenzi wathu ndi iye komanso zomwe zingativulaze. Munkhaniyi, tikambirana mayankho a mafunso awa: Kodi n’chifukwa chiyani timafunika kutetezedwa? Kodi Yehova amatiteteza bwanji? Komanso, kodi tiyenera kuchita chiyani kuti Yehova azitithandiza?