Mawu a M'munsi
a Munkhaniyi, tiona mmene kukonda Yehova, Akhristu anzathu ngakhalenso adani athu, kungatithandizire kupirira anthu ena mādzikoli akamadana nafe. Tionanso chifukwa chake Yesu ananena kuti tikhoza kukhala osangalala ngakhale anthu ena azidana nafe.